Mateyu 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kaya mukhulupirira kapena ayi, Yohane ndiye ‘Eliya woyembekezeka kubwera uja.’+ Mateyu 17:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ophunzirawo anamufunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya ayenera kubwera choyamba?”+
10 Koma ophunzirawo anamufunsa kuti: “Nanga n’chifukwa chiyani alembi amanena kuti Eliya ayenera kubwera choyamba?”+