Yohane 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Simoni Petulo anati: “Ine ndikupita kukapha nsomba.” Enawonso anati: “Ifenso tipita nawe.” Iwo anapitadi ndi kukwera ngalawa, koma mkati mwa usiku umenewo sanaphe kanthu.+
3 Ndiyeno Simoni Petulo anati: “Ine ndikupita kukapha nsomba.” Enawonso anati: “Ifenso tipita nawe.” Iwo anapitadi ndi kukwera ngalawa, koma mkati mwa usiku umenewo sanaphe kanthu.+