Malaki 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzatembenuza mitima ya abambo kuti ikhale ngati ya ana, ndipo adzatembenuza mitima ya ana kuti ikhale ngati ya abambo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.”+
6 Iye adzatembenuza mitima ya abambo kuti ikhale ngati ya ana, ndipo adzatembenuza mitima ya ana kuti ikhale ngati ya abambo.* Adzachita zimenezi kuti ine ndisabwere kudzawononga dziko lapansi.”+