Luka 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Koma mtsogoleri wa sunagoge ataona izi, anakwiya chifukwa Yesu anachiritsa munthu pa sabata.+ Choncho anayamba kuuza khamu la anthu kuti: “Pali masiku 6 oyenera kugwira ntchito. Muzibwera masiku amenewo kudzachiritsidwa, osati tsiku la sabata.”+ Yohane 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ena mwa Afarisiwo anayamba kunena kuti: “Munthu ameneyu si wochokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata.”+ Ena anayamba kunena kuti: “Koma munthu wochimwa angachite bwanji zizindikiro+ zoterezi?” Choncho panakhala kugawanika+ pakati pawo.
14 Koma mtsogoleri wa sunagoge ataona izi, anakwiya chifukwa Yesu anachiritsa munthu pa sabata.+ Choncho anayamba kuuza khamu la anthu kuti: “Pali masiku 6 oyenera kugwira ntchito. Muzibwera masiku amenewo kudzachiritsidwa, osati tsiku la sabata.”+
16 Ena mwa Afarisiwo anayamba kunena kuti: “Munthu ameneyu si wochokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata.”+ Ena anayamba kunena kuti: “Koma munthu wochimwa angachite bwanji zizindikiro+ zoterezi?” Choncho panakhala kugawanika+ pakati pawo.