Maliko 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Choncho Afarisi anali kumuyang’anitsitsa kuti aone ngati angachiritse munthuyo pa sabata, n’cholinga chakuti amuimbe mlandu.+
2 Choncho Afarisi anali kumuyang’anitsitsa kuti aone ngati angachiritse munthuyo pa sabata, n’cholinga chakuti amuimbe mlandu.+