Mateyu 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mmenemo munali munthu wopuwala dzanja.+ Chotero iwo anam’funsa kuti, “Kodi n’kololeka kuchiritsa odwala tsiku la sabata?” Cholinga chawo chinali kum’peza chifukwa, kuti amuzenge mlandu.+ Luka 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Alembi ndi Afarisi anali kumuyang’anitsitsa+ tsopano, kuti aone ngati angachiritse munthu pa sabata. Iwo anali n’cholinga chakuti am’peze chifukwa.+ Luka 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kanthawi kena atalowa m’nyumba ya mmodzi wa akuluakulu a Afarisi pa sabata kukadya chakudya,+ Afarisiwo anali kumuyang’anitsitsa.+
10 Mmenemo munali munthu wopuwala dzanja.+ Chotero iwo anam’funsa kuti, “Kodi n’kololeka kuchiritsa odwala tsiku la sabata?” Cholinga chawo chinali kum’peza chifukwa, kuti amuzenge mlandu.+
7 Alembi ndi Afarisi anali kumuyang’anitsitsa+ tsopano, kuti aone ngati angachiritse munthu pa sabata. Iwo anali n’cholinga chakuti am’peze chifukwa.+
14 Kanthawi kena atalowa m’nyumba ya mmodzi wa akuluakulu a Afarisi pa sabata kukadya chakudya,+ Afarisiwo anali kumuyang’anitsitsa.+