Maliko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kachiwirinso Yesu analowa m’sunagoge. Mmenemo munali munthu wa dzanja lopuwala.+ Luka 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsiku linanso la sabata,+ iye analowa m’sunagoge n’kuyamba kuphunzitsa. Mmenemo munali munthu amene dzanja lake lamanja linali lopuwala.+
6 Tsiku linanso la sabata,+ iye analowa m’sunagoge n’kuyamba kuphunzitsa. Mmenemo munali munthu amene dzanja lake lamanja linali lopuwala.+