Mateyu 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mmenemo munali munthu wopuwala dzanja.+ Chotero iwo anam’funsa kuti, “Kodi n’kololeka kuchiritsa odwala tsiku la sabata?” Cholinga chawo chinali kum’peza chifukwa, kuti amuzenge mlandu.+ Maliko 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kachiwirinso Yesu analowa m’sunagoge. Mmenemo munali munthu wa dzanja lopuwala.+
10 Mmenemo munali munthu wopuwala dzanja.+ Chotero iwo anam’funsa kuti, “Kodi n’kololeka kuchiritsa odwala tsiku la sabata?” Cholinga chawo chinali kum’peza chifukwa, kuti amuzenge mlandu.+