Mateyu 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mmenemo munali munthu wolumala dzanja.+ Choncho iwo anamufunsa kuti, “Kodi nʼzololeka kuchiritsa odwala pa tsiku la Sabata?” Cholinga chawo chinali choti amupezere chifukwa nʼkumuimba mlandu.+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:10 Yesu—Ndi Njira, tsa. 78 Nsanja ya Olonda,8/1/1998, ptsa. 9-101/1/1987, tsa. 14
10 Mmenemo munali munthu wolumala dzanja.+ Choncho iwo anamufunsa kuti, “Kodi nʼzololeka kuchiritsa odwala pa tsiku la Sabata?” Cholinga chawo chinali choti amupezere chifukwa nʼkumuimba mlandu.+