Deuteronomo 15:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Wina mwa abale ako akasauka pakati panu, mu umodzi mwa mizinda yanu, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, usamuumire mtima kapena kumuumitsira dzanja lako.+ Miyambo 3:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+ Miyambo 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Tsiku lonse amaoneka kuti akulakalaka kwambiri chinachake, koma wolungama amapatsa ndipo saumira chilichonse.+ Mateyu 5:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Munthu akakupempha kanthu m’patse, ndipo munthu wofuna kukongola kanthu kwa iwe popanda chiwongoladzanja usamukanize.+
7 “Wina mwa abale ako akasauka pakati panu, mu umodzi mwa mizinda yanu, m’dziko limene Yehova Mulungu wako akukupatsa, usamuumire mtima kapena kumuumitsira dzanja lako.+
27 Usalephere kuchitira zabwino anthu amene akufunikira zabwinozo,+ pamene dzanja lako lingathe kuchita zimenezo.+
26 Tsiku lonse amaoneka kuti akulakalaka kwambiri chinachake, koma wolungama amapatsa ndipo saumira chilichonse.+
42 Munthu akakupempha kanthu m’patse, ndipo munthu wofuna kukongola kanthu kwa iwe popanda chiwongoladzanja usamukanize.+