-
Mateyu 8:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 kuti: “Ambuye, wantchito wanga wafa ziwalo moti ali gone m’nyumba, ndipo akuzunzika koopsa.”
-
-
Yohane 4:47Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
47 Munthuyu atamva kuti Yesu wafika ku Galileya kuchokera ku Yudeya, anapita kwa iye ndi kuyamba kumupempha kuti apiteko ndi kukachiritsa mwana wakeyo, pakuti anali pafupi kumwalira.
-