Luka 8:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Koma anthu onse anali kulira ndi kudziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni. Choncho Yesu anawauza kuti: “Tontholani,+ pakuti mwanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Yohane 11:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ndipo Yesu atamuona akulira, ndi Ayuda amene anabwera naye pamodzi akuliranso, anadzuma povutika mumtima ndi kumva chisoni.+
52 Koma anthu onse anali kulira ndi kudziguguda pachifuwa chifukwa cha chisoni. Choncho Yesu anawauza kuti: “Tontholani,+ pakuti mwanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+
33 Ndipo Yesu atamuona akulira, ndi Ayuda amene anabwera naye pamodzi akuliranso, anadzuma povutika mumtima ndi kumva chisoni.+