Luka 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamene Ambuye anaona mayiwo, anawamvera chifundo,+ ndipo anawauza kuti: “Tontholani mayi.”+