Mateyu 13:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi? Yohane 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Abale akewo+ sanali kumukhulupirira.+ Machitidwe 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mogwirizana, onsewa analimbikira kupemphera,+ pamodzi ndi amayi ena+ komanso Mariya mayi a Yesu, limodzinso ndi abale ake a Yesu.+
55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?
14 Mogwirizana, onsewa analimbikira kupemphera,+ pamodzi ndi amayi ena+ komanso Mariya mayi a Yesu, limodzinso ndi abale ake a Yesu.+