Mateyu 13:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi? Yohane 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Abale akewo+ sanali kumukhulupirira.+ Agalatiya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma sindinaone mtumwi winanso kupatulapo Yakobo,+ m’bale+ wa Ambuye.
55 Kodi si mwana wa mmisiri wamatabwa uyu?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo abale ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?