Yesaya 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho Yehovayo akupatsani chizindikiro anthu inu: Tamverani! Mtsikana+ adzatenga pakati+ ndipo adzabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli. Mateyu 1:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Koma sanagone+ naye mpaka anabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo anamutcha dzina lakuti Yesu.+
14 Choncho Yehovayo akupatsani chizindikiro anthu inu: Tamverani! Mtsikana+ adzatenga pakati+ ndipo adzabereka mwana wamwamuna.+ Mwanayo adzam’patsa dzina lakuti Emanueli.