Mateyu 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Mukalowa mumzinda kapena m’mudzi uliwonse, fufuzani mmenemo yemwe ali woyenerera, ndipo mukhalebe momwemo kufikira nthawi yochoka.+ Maliko 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso anawauza kuti: “Mukafika pakhomo lililonse,+ khalani pamenepo mpaka nthawi yochoka kumeneko itakwana.+ Luka 10:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mukafika panyumba, choyamba muzinena kuti, ‘Mtendere ukhale panyumba pano.’+ Luka 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Choncho khalani m’nyumba yamtendereyo.+ Muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako n’kupita kunyumba zina.+
11 “Mukalowa mumzinda kapena m’mudzi uliwonse, fufuzani mmenemo yemwe ali woyenerera, ndipo mukhalebe momwemo kufikira nthawi yochoka.+
10 Komanso anawauza kuti: “Mukafika pakhomo lililonse,+ khalani pamenepo mpaka nthawi yochoka kumeneko itakwana.+
7 Choncho khalani m’nyumba yamtendereyo.+ Muzidya ndi kumwa zimene angakupatseni,+ chifukwa wantchito ayenera kulandira malipiro ake.+ Musamachoke kumene mwafikirako n’kupita kunyumba zina.+