Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 M’bale wangayo mukamuuze kuti, ‘Mtendere ukhale nawe+ pamodzi ndi onse a m’nyumba yako ndi zonse zimene uli nazo.

  • Mateyu 10:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamene mukulowa m’nyumba, perekani moni kwa a m’banja limenelo.

  • Luka 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Koma mukafika pakhomo lililonse, khalani pamenepo kufikira nthawi yochoka kumeneko.+

  • Yohane 20:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Pa tsiku limenelo, tsiku loyamba la mlunguwo,+ ophunzirawo anasonkhana pamodzi madzulo. Iwo anali atakhoma zitseko m’nyumba imene analimo chifukwa choopa+ Ayuda, ndipo Yesu anafika+ n’kuimirira pakati pawo ndi kunena kuti: “Mtendere ukhale nanu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena