Mateyu 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndithu ndikukuuzani kuti pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe kufikira choyamba ataona Mwana wa munthu akubwera monga mfumu.”+ Maliko 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndiye anawauzanso kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe, kufikira choyamba ataona ufumu wa Mulungu utabwera ndi mphamvu zake.”+
28 Ndithu ndikukuuzani kuti pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe kufikira choyamba ataona Mwana wa munthu akubwera monga mfumu.”+
9 Ndiye anawauzanso kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe, kufikira choyamba ataona ufumu wa Mulungu utabwera ndi mphamvu zake.”+