Mateyu 16:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndithu ndikukuuzani kuti pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe kufikira choyamba ataona Mwana wa munthu akubwera monga mfumu.”+ Luka 9:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma ndikukuuzani ndithu, Pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe kufikira choyamba ataona ufumu wa Mulungu.”+ 1 Akorinto 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pakuti ufumu wa Mulungu sunagone m’mawu, koma mu mphamvu.+
28 Ndithu ndikukuuzani kuti pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe kufikira choyamba ataona Mwana wa munthu akubwera monga mfumu.”+
27 Koma ndikukuuzani ndithu, Pali ena mwa amene aimirira pano amene sadzalawa imfa m’pang’ono pomwe kufikira choyamba ataona ufumu wa Mulungu.”+