-
1 Atesalonika 1:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Chifukwa pamene tinali kulalikira uthenga wabwino kwa inu, sitinali kungolankhula basi, koma uthengawo unakukhudzani kwambiri, komanso unabwera limodzi ndi mphamvu+ ya mzimu woyera, ndipo unachititsa kuti mukhale otsimikiza+ mtima kwambiri. Ndipo inuyo mukudziwa zimene tinakuchitirani pofuna kukuthandizani.+
-