Luka 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako anati: “Mwana wa munthu ayenera kukumana ndi mavuto ambiri. Iye adzakanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno adzaphedwa,+ koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+ Luka 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Komabe ndiyenera kupitiriza ulendo wanga lero ndi mawa ndi tsiku linalo, chifukwa n’kosayenera kuti mneneri amuphere kunja kwa Yerusalemu.+
22 Kenako anati: “Mwana wa munthu ayenera kukumana ndi mavuto ambiri. Iye adzakanidwa ndi akulu, ansembe aakulu ndi alembi. Ndiyeno adzaphedwa,+ koma pa tsiku lachitatu adzaukitsidwa.”+
33 Komabe ndiyenera kupitiriza ulendo wanga lero ndi mawa ndi tsiku linalo, chifukwa n’kosayenera kuti mneneri amuphere kunja kwa Yerusalemu.+