Mateyu 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano atafika kufupi ndi khamu la anthu,+ mwamuna wina anamuyandikira, ndipo anam’gwadira ndi kunena kuti: Maliko 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano atayandikira kumene kunali ophunzira ena aja, iwo anaona khamu lalikulu la anthu litawazungulira, ndipo alembi anali kukangana nawo.+
14 Tsopano atafika kufupi ndi khamu la anthu,+ mwamuna wina anamuyandikira, ndipo anam’gwadira ndi kunena kuti:
14 Tsopano atayandikira kumene kunali ophunzira ena aja, iwo anaona khamu lalikulu la anthu litawazungulira, ndipo alembi anali kukangana nawo.+