Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Amene sali kumbali yanga ndi wotsutsana ndi ine, ndipo amene sagwira limodzi ndi ine ntchito yosonkhanitsa anthu kwa ine amawabalalitsa.+

  • Luka 11:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Amene sali kumbali yanga akutsutsana ndi ine, ndipo amene sasonkhanitsa anthu pamodzi ndi ine amawabalalitsa.+

  • 1 Akorinto 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho ndikufuna mudziwe kuti palibe wolankhula mwa mzimu wa Mulungu amene anganene kuti: “Yesu ndi wotembereredwa!”+ Palibenso amene anganene popanda mzimu woyera kuti: “Yesu ndiye Ambuye!”+

  • Afilipi 1:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Akatero ndiye kuti achita chiyani? Palibe! Mulimonse mmene zingakhalire, kaya ndi mwachiphamaso+ kapena m’choonadi, Khristu akufalitsidwabe.+ Choncho ine ndikukondwera. Ndipotu ndipitiriza kukondwera,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena