Aefeso 2:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+ 1 Timoteyo 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Koma amene amatsatira zilakolako zake kuti azikhutiritse,+ ndi wakufa+ ngakhale kuti ali ndi moyo.
2 Ndiponso, Mulungu anapangitsa inuyo kukhala amoyo pamene munali akufa chifukwa cha zolakwa zanu ndi machimo anu.+