Machitidwe 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anakhala akuchita zimenezi kwa masiku ambiri. Potsirizira pake Paulo anatopa nazo+ ndipo anatembenuka n’kuuza mzimuwo kuti: “Ndikukulamula m’dzina la Yesu Khristu kuti utuluke mwa mtsikanayu.”+ Nthawi yomweyo mzimuwo unatuluka.+
18 Iye anakhala akuchita zimenezi kwa masiku ambiri. Potsirizira pake Paulo anatopa nazo+ ndipo anatembenuka n’kuuza mzimuwo kuti: “Ndikukulamula m’dzina la Yesu Khristu kuti utuluke mwa mtsikanayu.”+ Nthawi yomweyo mzimuwo unatuluka.+