Maliko 1:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho Yesu anachiritsa ambiri amene anali kudwala matenda osiyanasiyana,+ ndipo anatulutsa ziwanda zambiri. Koma sanalole kuti ziwandazo zilankhule, chifukwa zinali kum’dziwa kuti ndi Khristu.+ Luka 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja ndi kuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse ndi kuti azitha kuchiritsa matenda.+ Luka 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Tsopano anthu okwana 70 aja anabwerera ali osangalala. Iwo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zinatigonjera+ pamene tinagwiritsa ntchito dzina lanu.”
34 Choncho Yesu anachiritsa ambiri amene anali kudwala matenda osiyanasiyana,+ ndipo anatulutsa ziwanda zambiri. Koma sanalole kuti ziwandazo zilankhule, chifukwa zinali kum’dziwa kuti ndi Khristu.+
9 Tsopano Yesu anasonkhanitsa atumwi 12 aja ndi kuwapatsa mphamvu ndi ulamuliro pa ziwanda zonse ndi kuti azitha kuchiritsa matenda.+
17 Tsopano anthu okwana 70 aja anabwerera ali osangalala. Iwo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zinatigonjera+ pamene tinagwiritsa ntchito dzina lanu.”