Luka 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako anthu okwana 70 aja anabwerera akusangalala ndipo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zimatigonjera tikagwiritsa ntchito dzina lanu.”+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:17 Nsanja ya Olonda,7/1/1988, tsa. 17
17 Kenako anthu okwana 70 aja anabwerera akusangalala ndipo anauza Yesu kuti: “Ambuye, ngakhale ziwanda zimatigonjera tikagwiritsa ntchito dzina lanu.”+