Mateyu 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Koma inu ndinu odala chifukwa maso anu amaona,+ komanso makutu anu amamva.