Mateyu 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma inu ndinu osangalala chifukwa maso anu amaona komanso makutu anu amamva.+