-
Luka 10:23, 24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Ndiyeno Yesu ndi ophunzira akewo ali kwaokha, anawauza kuti: “Osangalala ndi anthu amene akuona zimene inu mukuonazi.+ 24 Chifukwa ndithu ndikukuuzani, aneneri ambiri komanso mafumu ankalakalaka kuti aone zinthu zimene mukuziona inuzi koma sanazione,+ komanso kuti amve zimene mukumva inuzi koma sanazimve.”
-