1 Akorinto 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma monga mmene Malemba amanenera: “Palibe munthu amene anaonapo kapena kumvapo kapenanso kuganizapo zimene Mulungu wakonzera omukonda.”+ 1 Petulo 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Aneneri amene analosera+ za kukoma mtima kwakukulu kumene munali kudzasonyezedwa,+ anafufuza za chipulumutso chimenechi mwakhama ndi mosamala.+
9 Koma monga mmene Malemba amanenera: “Palibe munthu amene anaonapo kapena kumvapo kapenanso kuganizapo zimene Mulungu wakonzera omukonda.”+
10 Aneneri amene analosera+ za kukoma mtima kwakukulu kumene munali kudzasonyezedwa,+ anafufuza za chipulumutso chimenechi mwakhama ndi mosamala.+