Luka 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo iye anawauza kuti: “Inu mumadzitcha olungama pamaso pa anthu,+ koma Mulungu akudziwa mitima yanu.+ Chifukwa chimene chili chapamwamba kwa anthu n’chonyansa m’maso mwa Mulungu.+
15 Pamenepo iye anawauza kuti: “Inu mumadzitcha olungama pamaso pa anthu,+ koma Mulungu akudziwa mitima yanu.+ Chifukwa chimene chili chapamwamba kwa anthu n’chonyansa m’maso mwa Mulungu.+