Salimo 37:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+ Yesaya 51:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Yemwe wawerama atamangidwa maunyolo adzamasulidwa msangamsanga.+ Iye sadzafa, sadzatsikira kudzenje,+ komanso sadzasowa chakudya.+
25 Ndinali mwana, ndipo tsopano ndakula,+Koma sindinaonepo munthu aliyense wolungama atasiyidwa,+Kapena ana ake akupemphapempha chakudya.+
14 “Yemwe wawerama atamangidwa maunyolo adzamasulidwa msangamsanga.+ Iye sadzafa, sadzatsikira kudzenje,+ komanso sadzasowa chakudya.+