Mateyu 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma ngati diso lako lili loipa,+ thupi lako lonse lidzachita mdima. Choncho ngati kuwala kumene kuli mwa iwe ndiko mdima, ndiye kuti mdimawo ndi wandiweyani!+
23 Koma ngati diso lako lili loipa,+ thupi lako lonse lidzachita mdima. Choncho ngati kuwala kumene kuli mwa iwe ndiko mdima, ndiye kuti mdimawo ndi wandiweyani!+