Mateyu 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Khalani maso ndipo samalani ndi chofufumitsa cha Afarisi ndi Asaduki.”+ Maliko 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndipo anayamba kuwachenjeza mwamphamvu kuti: “Khalani maso! Chenjerani ndi chofufumitsa cha Afarisi ndi cha Herode.”+
6 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Khalani maso ndipo samalani ndi chofufumitsa cha Afarisi ndi Asaduki.”+
15 Ndipo anayamba kuwachenjeza mwamphamvu kuti: “Khalani maso! Chenjerani ndi chofufumitsa cha Afarisi ndi cha Herode.”+