Mateyu 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Khalani maso ndipo samalani ndi chofufumitsa cha Afarisi ndi Asaduki.”+ Luka 12:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyi, chikhamu cha anthu masauzandemasauzande chinali chitasonkhana, moti anali kupondanapondana. Pamenepo Yesu anayamba kulankhula ndi ophunzira ake choyamba kuti: “Samalani ndi chofufumitsa+ cha Afarisi, chimene chili chinyengo.+ 1 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+ Agalatiya 5:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chofufumitsa chaching’ono chimafufumitsa mtanda wonse.+
6 Ndiyeno Yesu anawauza kuti: “Khalani maso ndipo samalani ndi chofufumitsa cha Afarisi ndi Asaduki.”+
12 Pa nthawiyi, chikhamu cha anthu masauzandemasauzande chinali chitasonkhana, moti anali kupondanapondana. Pamenepo Yesu anayamba kulankhula ndi ophunzira ake choyamba kuti: “Samalani ndi chofufumitsa+ cha Afarisi, chimene chili chinyengo.+
7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+