Yesaya 44:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Kumbukira zinthu zimenezi iwe Yakobo,+ ndiponso iwe Isiraeli, pakuti ndiwe mtumiki wanga.+ Ine ndiye amene ndinakuumba.+ Iweyo ndiwe mtumiki wanga. Iwe Isiraeli, ine sindikuiwala.+
21 “Kumbukira zinthu zimenezi iwe Yakobo,+ ndiponso iwe Isiraeli, pakuti ndiwe mtumiki wanga.+ Ine ndiye amene ndinakuumba.+ Iweyo ndiwe mtumiki wanga. Iwe Isiraeli, ine sindikuiwala.+