Mateyu 20:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yesu anayankha kuti: “Anthu inu simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe+ zimene ine ndatsala pang’ono kumwa?” Iwo anati: “Inde tingamwe.” Maliko 10:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma Yesu anawauza kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungathe kumwa zimene ine ndikumwa, kapena kubatizidwa ubatizo umene ine ndikubatizidwa nawo?”+ Yohane 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Moyo wanga ukusautsika tsopano,+ ndinene chiyani kodi? Atate ndipulumutseni ku nthawi yosautsayi.+ Komabe nthawi imeneyi iyenera kundifikira pakuti ndiye chifukwa chake ndinabwera.
22 Koma Yesu anayankha kuti: “Anthu inu simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungamwe+ zimene ine ndatsala pang’ono kumwa?” Iwo anati: “Inde tingamwe.”
38 Koma Yesu anawauza kuti: “Simukudziwa chimene mukupempha. Kodi mungathe kumwa zimene ine ndikumwa, kapena kubatizidwa ubatizo umene ine ndikubatizidwa nawo?”+
27 Moyo wanga ukusautsika tsopano,+ ndinene chiyani kodi? Atate ndipulumutseni ku nthawi yosautsayi.+ Komabe nthawi imeneyi iyenera kundifikira pakuti ndiye chifukwa chake ndinabwera.