Mateyu 21:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako anaona mkuyu m’mbali mwa msewu ndipo atapita pomwepo, sanapezemo chilichonse+ koma masamba okhaokha. Choncho anauza mtengowo kuti: “Kuyambira lero sudzabalanso zipatso kwamuyaya.”+ Ndipo mkuyuwo unafota nthawi yomweyo.
19 Kenako anaona mkuyu m’mbali mwa msewu ndipo atapita pomwepo, sanapezemo chilichonse+ koma masamba okhaokha. Choncho anauza mtengowo kuti: “Kuyambira lero sudzabalanso zipatso kwamuyaya.”+ Ndipo mkuyuwo unafota nthawi yomweyo.