Maliko 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo ali chapatali ndithu, anaona mkuyu umene unali ndi masamba. Iye anapita pomwepo kuti akaone ngati angapezemo kanthu. Koma atafika pamtengowo, sanapezemo chilichonse koma masamba okha basi, pakuti sinali nyengo ya nkhuyu.+ Luka 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anayamba kufotokoza fanizo ili: “Munthu wina anali ndi mkuyu m’munda wake wa mpesa,+ ndipo anapita kukafuna chipatso mumtengowo,+ koma sanapezemo chilichonse.+
13 Ndipo ali chapatali ndithu, anaona mkuyu umene unali ndi masamba. Iye anapita pomwepo kuti akaone ngati angapezemo kanthu. Koma atafika pamtengowo, sanapezemo chilichonse koma masamba okha basi, pakuti sinali nyengo ya nkhuyu.+
6 Kenako anayamba kufotokoza fanizo ili: “Munthu wina anali ndi mkuyu m’munda wake wa mpesa,+ ndipo anapita kukafuna chipatso mumtengowo,+ koma sanapezemo chilichonse.+