-
Habakuku 3:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ngakhale mkuyu usaphukire maluwa,+ mtengo wa mpesa usabale zipatso, mtengo wa maolivi ulephere kubala zipatso, munda wa m’mphepete mwa phiri usatulutse chakudya,+ nkhosa ndi ng’ombe zithemo m’khola,+
-