Mateyu 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Koma ambiri amene ali oyamba adzakhala omaliza, ndipo omaliza adzakhala oyamba.+ Maliko 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma ambiri amene ali oyamba adzakhala omaliza, ndipo omaliza adzakhala oyamba.”+