Mateyu 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Koma ambiri amene ali oyamba adzakhala omaliza, ndipo omaliza adzakhala oyamba.+ Mateyu 20:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho omalizira adzakhala oyambirira ndipo oyambirira adzakhala omalizira.”+ Luka 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndithudi amene ali omalizira adzakhala oyamba, ndipo oyamba adzakhala omalizira.”+