Mateyu 19:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Koma ambiri amene ali oyamba adzakhala omaliza, ndipo omaliza adzakhala oyamba.+ Maliko 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Choncho anakhala pansi ndi kuitana ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Ngati aliyense akufuna kukhala woyamba, ayenera kukhala wotsiriza pa onse, ndiponso mtumiki wa onse.”+ Maliko 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma ambiri amene ali oyamba adzakhala omaliza, ndipo omaliza adzakhala oyamba.”+ Luka 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ndithudi amene ali omalizira adzakhala oyamba, ndipo oyamba adzakhala omalizira.”+
35 Choncho anakhala pansi ndi kuitana ophunzira 12 aja ndi kuwauza kuti: “Ngati aliyense akufuna kukhala woyamba, ayenera kukhala wotsiriza pa onse, ndiponso mtumiki wa onse.”+