Luka 13:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Komanso, anthu adzabwera kuchokera kumbali za kum’mawa ndi kumadzulo, kumpoto ndi kum’mwera,+ ndipo adzadya patebulo mu ufumu wa Mulungu.+ Chivumbulutso 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+
29 Komanso, anthu adzabwera kuchokera kumbali za kum’mawa ndi kumadzulo, kumpoto ndi kum’mwera,+ ndipo adzadya patebulo mu ufumu wa Mulungu.+
9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+