Deuteronomo 24:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Mwamuna akatenga mkazi watsopano,+ sayenera kukhala m’gulu lankhondo, ndiponso asakakamizidwe kuchita china chilichonse. Akhale kunyumba osachita zinthu zimenezi kwa chaka chimodzi kuti asangalatse mkazi amene watenga.+ 1 Akorinto 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma mwamuna wokwatira amadera nkhawa+ zinthu za dziko, mmene angakondweretsere mkazi wake,+
5 “Mwamuna akatenga mkazi watsopano,+ sayenera kukhala m’gulu lankhondo, ndiponso asakakamizidwe kuchita china chilichonse. Akhale kunyumba osachita zinthu zimenezi kwa chaka chimodzi kuti asangalatse mkazi amene watenga.+