Mateyu 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 “Kodi mukuganiza bwanji? Munthu wina anali ndi ana awiri.+ Ndipo anapita kwa mwana woyamba n’kumuuza kuti: ‘Mwana wanga, lero upite kukagwira ntchito m’munda wa mpesa.’
28 “Kodi mukuganiza bwanji? Munthu wina anali ndi ana awiri.+ Ndipo anapita kwa mwana woyamba n’kumuuza kuti: ‘Mwana wanga, lero upite kukagwira ntchito m’munda wa mpesa.’