Maliko 14:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Koma iye anakana kuti: “Ngakhale kumudziwa, sindikumudziwa ameneyo, ndipo sindikumvetsa kuti ukunena chiyani.” Atatero anatuluka panja ndi kupita kukachipinda ka kuchipata.+ Yohane 18:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+
68 Koma iye anakana kuti: “Ngakhale kumudziwa, sindikumudziwa ameneyo, ndipo sindikumvetsa kuti ukunena chiyani.” Atatero anatuluka panja ndi kupita kukachipinda ka kuchipata.+
25 Pa nthawiyi Simoni Petulo anali ataimirira akuwotha moto. Pamenepo iwo anamufunsa kuti: “Kodi iwenso si iwe mmodzi wa ophunzira ake?” Iye anakana n’kunena kuti: “Ayi si ine.”+