Yohane 18:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Simoni Petulo, popeza anali ndi lupanga, analisolola ndi kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe ndi kuduliratu khutu lake lakumanja.+ Dzina la kapoloyo anali Makasi.
10 Pamenepo Simoni Petulo, popeza anali ndi lupanga, analisolola ndi kutema nalo kapolo wa mkulu wa ansembe ndi kuduliratu khutu lake lakumanja.+ Dzina la kapoloyo anali Makasi.